1 Kings 1:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma sadaitaneko mneneri Natani, Benaya, anthu amphamvu aja a mfumu Davide, kapenanso Solomoni mbale wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma Natani mneneriyo, ndi Benaya, ndi anthu amphamvu aja, ndi Solomoni mbale wake, sanawaitane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma sanayitane mneneri Natani kapena Benaya kapenanso asilikali amphamvu a Davide ngakhalenso mʼbale wake Solomoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma Natani mneneriyo, ndi Benaya, ndi anthu amphamvu aja, ndi Solomo mbale wace, sanawaitana.