1 Kings 1:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Natani adafunsa Bateseba, mai wa Solomoni, kuti, “Kodi simudamve kuti Adoniya, mwana wa Hagiti, wadzilonga ufumu, chikhalirecho Davide mbuyathu sakuzidziŵa zimenezo?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Natani ananena ndi Bateseba amake wa Solomoni, nati, Kodi sunamva kuti Adoniya mwana wa Hagiti walowa ufumu, ndipo Davide mbuye wathu sadziwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Natani anafunsa Batiseba, amayi ake a Solomoni, kuti, “Kodi simunamve kuti Adoniya, mwana wa Hagiti, walowa ufumu popanda Davide mbuye wathu kudziwa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Natani ananena ndi Batiseba amace wa Solomo, nati, Kodi sunamva kuti Adoniya mwana wa Hagiti walowa ufumu, ndipo Davide mbuye wathu sadziwa?