1 Kings 1:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono ndikupatseni nzeru kuti mupulumutse moyo wanu pamodzi ndi moyo wa mwana wanu Solomoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ubwere tsono, ndikupangire, kuti usunge moyo wako, ndi moyo wa mwana wako Solomoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano ine ndikulangizeni inu mmene mungapulumutsire moyo wanu ndi moyo wa mwana wanu Solomoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ubwere tsono, ndikupangire, kuti usunge moyo wako, ndi moyo wa mwana wako Solomo.