1 Kings 1:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bateseba adagwada nalambira mfumu. Tsono mfumu idamufunsa kuti, “Kodi nkwabwino?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Bateseba anawerama nalambira mfumu, ndi mfumu niti, Ufunanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Batiseba anagwada nalambira mfumu. Mfumu inamufunsa kuti, “Kodi nʼchiyani chimene ukufuna?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Batiseba anawerama nalambira mfumu, ndi mfumu niti, Ufunanji?