1 Kings 1:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukapanda kutero, zidzachitike nzakuti inu mbuyanga mutatisiya, kulondola kumene kudapita makolo anu, ine pamodzi ndi mwana wanga Solomoni adzatiyesa ogalukira mfumu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukapanda kutero, kudzachitika, pamene mbuye wanga mfumu atagona kwa makolo ake, ine ndi mwana wanga Solomoni tidzayesedwa ochimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukapanda kutero, mbuye wanga, mukadzangotisiya nʼkulondola kumene kunapita makolo anu, ine pamodzi ndi mwana wangayu Solomoni adzatiyesa owukira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukapanda kutero, kudzacitika, pamene mbuye wanga mfumu atagona kwa makolo ace, ine ndi mwana wanga Solomo tidzayesedwa ocimwa.