1 Kings 1:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adauza mfumu kuti, “Kwafika mneneri Natani.” Tsono iye atafika pamaso pa mfumu, adaŵeramitsa mutu wake pansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anauza mfumu, kuti, Wafika Natani mneneriyo. Ndipo iye anafika pamaso pa mfumu, naweramitsa nkhope yake pansi pamaso pa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anthu anawuza mfumu kuti, “Kwabwera mneneri Natani.” Kotero iye anafika pamaso pa mfumu ndipo anawerama nagunditsa nkhope yake pansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anauza mfumu, kuti, Wafika Natani mneneriyo. Ndipo iye anafika pamaso pa mfumu, naweramitsa nkhope yace pansi pamaso pa mfumu.