1 Kings 1:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine mtumiki wanu, wansembe Zadoki ndi Benaya mwana wa Yehoyada, ndiponso Solomoni mwana wanu, tonsefe sadatiitaneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine, inde inedi mnyamata wanu, ndi Zadoki wansembe, ndi Benaya mwana wa Yehoyada, ndi Solomoni mnyamata wanu, sanatiitane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ine kapolo wanu, wansembe Zadoki ndi Benaya mwana wa Yehoyada, ndiponso kapolo wanu Solomoni sanatiyitane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine, inde inedi mnyamata wanu, ndi Zadoki wansembe, ndi Benaya mwana wa Yehoyada, ndi Solomo mnyamata wanu, sanatiitana.