1 Kings 1:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
monga momwe ndidaakulonjezera molumbira m'dzina la Chauta, Mulungu wa Israele, kuti mwana wako Solomoni ndiye amene adzaloŵe ufumu ndi kukhala pa mpando wanga, m'malo mwanga, ndikubwerezanso zomwezo lero.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
zedi monga umo ndinalumbirira iwe pa Yehova Mulungu wa Israele, ndi kuti, Zoonadi Solomoni mwana wako adzakhala mfumu nditamuka ine, nadzakhala pa mpando wanga wachifumu m'malo mwa ine, zedi nditero lero lomwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndithu ine lero ndichita zonse zimene ndinalumbira kwa Yehova Mulungu wa Israeli kuti, mwana wako Solomoni adzakhala mfumu mʼmalo mwanga ndipo adzakhala pa mpando wanga waufumu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
zedi monga umo ndinalumbirira iwe pa Yehova Mulungu wa Israyeli, ndi kuti, Zoonadi Solomo mwana wako adzakhala mfumu nditamuka ine, nadzakhala pa mpando wanga wacifumu m'malo mwa ine, zedi nditero lero lomwe.