1 Kings 1:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo Bateseba adaŵeramitsa mutu wake pansi nalambira mfumu, nati, “Mbuyanga mfumu Davide akhale ndi moyo mpaka muyaya!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Bateseba anaweramitsa pansi nkhope yake, nalambira mfumu, nati, Mbuye wanga mfumu Davide akhale ndi moyo nthawi zamuyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Batiseba anawerama, nagunditsa mutu wake pansi nalambira mfumu, ndipo anati, “Mbuye wanga Mfumu Davide mukhale ndi moyo wautali!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Batiseba anaweramitsa pansi nkhope yace, nalambira mfumu, nati, Mbuye wanga mfumuakhale ndi moyo nthawi zamuyaya.