1 Kings 1:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu idaŵauza kuti, “Tengani anthu anga, ndipo mukweze Solomoni mwana wanga pa bulu wanga, mupite naye ku Gihoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inati kwa iwo, Tengani akapolo a mfumu yanu, nimukweze Solomoni mwana wanga pa nyuru yangayanga, nimutsikire naye ku Gihoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mfumuyo inati kwa iwo, “Tengani atumiki anga ndipo mukweze mwana wanga Solomoni pa bulu wanga ndipo mupite naye ku Gihoni. Mukalize lipenga ndi kufuwula kuti, ‘Akhale ndi moyo wautali mfumu Solomoni!’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inati kwa iwo, Tengani akapolo a mfumu yanu, nimukweze Solomo mwana wanga pa nyuru yanga yanga, nimutsikire naye ku Gihoni.