1 Kings 1:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo adapita namamtsatira pambuyo akuliza zitoliro ndi kukondwerera kwambiri, kotero kuti dziko lidagwedezeka chifukwa cha phokosolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse anakwera namtsata, naliza zitoliro, nakondwera ndi kukondwera kwakukulu, kotero kuti pansi panang'ambika ndi phokoso lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anthu onsewo anapita namutsatira pambuyo akuyimba zitoliro ndi kukondwerera kwambiri, kotero nthaka inagwedezeka chifukwa cha phokoso lawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse anakwera namtsata, naliza zitoliro, nakondwera ndi kukondwera kwakukuru, kotero kuti pansi panang'ambikandiphokosolao.