1 Kings 1:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akulankhulabe, adangoona Yonatani mwana wa wansembe Abiyatara wafika. Adoniya adamuuza kuti, “Loŵa, chifukwa ndiwe munthu wabwino, mwina mwake wabwera ndi uthenga wabwino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye akali chilankhulire, taona, walowa Yonatani mwana wa Abiyatara wansembe, ndipo Adoniya anati, Lowa, popeza ndiwe munthu wamphamvu, nubwera nao uthenga wabwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akuyankhula, Yonatani mwana wa wansembe Abiatara anafika. Adoniya anati, “Lowa. Munthu wabwino ngati iwe ayenera kubweretsa nkhani yabwino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iye akali cilankhulire, taona, walowa Yonatani mwana wa Abyatara wansembe, ndipo Adoniya anati, Lowa, popeza ndiwe munthu wamphamvu, nubwera nao uthenga wabwino.