1 Kings 1:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatuma wansembe Zadoki, mneneri Natani, ndi Benaya mwana wa Yehoyada ndiponso Akereti ndi Apeleti ku Gihoni. Ndipo iwo adamkweza Solomoniyo pa bulu wa mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo mfumu yatumanso Zadoki wansembe, ndi Natani mneneri, ndi Benaya mwana wa Yehoyada, ndi Akereti, ndi Apeleti aja, namkweza iye pa nyuru ya mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu yatuma Zadoki wansembe, mneneri Natani, Benaya mwana wa Yehoyada, Akereti ndi Apeleti ku Gihoni ndipo iwo amukweza pa bulu wa mfumu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo mfumu yatumanso Zadoki wansembe, ndi Natani mneneri, ndi Benaya mwana wa Yehoyada, ndi Akereti, ndi Apeleti aja, namkweza iye pa nyuru ya mfumu.