1 Kings 1:50 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Adoniya adayamba kuwopa Solomoni. Adapita ku Nyumba ya Mulungu nakagwira nsonga za guwa lansembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Adoniya anaopa chifukwa cha Solomoni, nanyamuka, nakagwira nyanga za guwa la nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Adoniya, poopa Solomoni, anapita ku Nyumba ya Mulungu nakagwira msonga za guwa lansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Adoniya anaopa cifukwa ca Solomo, nanyamuka, nakagwira nyanga za guwa la nsembe.