1 Kings 1:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bambo wake Davide anali asanamdzudzulepo nkamodzi komwe pomufunsa kuti, “Kodi zakutizakutizi ukuchitiranji?” Adoniyayo anali wokongola, ndipo adaapondana ndi Abisalomu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atate wake sadamvuta masiku ake onse, ndi kuti, Watero chifukwa ninji? Ndiponso anali munthu wokongola ndithu; napondana ndi Abisalomu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Abambo ake sanalowererepo nʼkamodzi komwe ndipo sanafunsepo kuti, “Nʼchifukwa chiyani ukuchita zimenezi?” Adoniyayo anali wokongola kwambiri ndipo anali wopondana ndi Abisalomu).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atate wace sadambvuta masiku ace onse, ndi kuti, Wlitero cifukwa ninji? Ndiponso anali munthu wokongola ndithu; napondana ndi Abisalomu.