1 Kings 1:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo adapangana ndi Yowabu, mwana wa Zeruya, ndiponso Abiyatara wansembe. Choncho iwowo adamtsata Adoniya namamthandiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapangana ndi Yowabu mwana wa Zeruya, ndi Abiyatara wansembeyo; ndipo amenewo anamtsata Adoniya namthandiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adoniya anagwirizana ndi Yowabu mwana wa Zeruya ndiponso Abiatara wansembe, ndipo iwowa anamuthandiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapangana ndi Yoabu mwana wa Zeruya, ndi Abyatara wansembeyo; ndipo amenewo anamtsata Adoniya namthandiza.