1 Kings 10:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu idapangitsanso mpando waukulu waufumu wa minyanga yanjovu, niwukuta ndi golide wabwino kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inapanga mpando waukulu wachifumu waminyanga, naukuta ndi golide woyengetsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inapangitsanso mpando waufumu waukulu wa minyanga ya njovu, ndipo inawukutira ndi golide wabwino kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inapanga mpando waukulu wacifumu waminyanga, naukuta ndi golidi woyengetsa.