1 Kings 10:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo anthu onse a pa dziko lapansi ankafunafuna kuti amuwone Solomoni ndi kumva nzeru zake zimene Mulungu adaaika mumtima mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse a pa dziko anafuna nkhope ya Solomoni, kudzamva nzeru zake zimene Mulungu analonga m'mtima mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse a dziko lapansi ankafunafuna kuyankhulana ndi Solomoni kuti amve nzeru zimene Mulungu anayika mu mtima mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse a pa dziko anafuna nkhope ya Solomo, kudzamva nzeru zace zimene Mulungu analonga m'mtima mwace.