1 Kings 10:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Solomoni ankagula akavalo ku Ejipito ndi ku Kuwe. Anthu amalonda a mfumu ankalandirira akavalo ku Kuwe, atapereka ndalama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akavalo a Solomoni anachokera ku Ejipito; anthu a malonda a mfumu anawagula magulumagulu, gulu lililonse mtengo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akavalo a Solomoni ankachokera ku Igupto komanso ku Kuwe. Anthu a malonda a mfumu ankatengera akavalowo ku Kuwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akavalo a Solomo anacokera ku Aigupto; anthu a malonda a mfumu anawagula magulu magulu, gulu liri lonse mtengo wace.