1 Kings 11:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yowabu ndi ankhondo ake adaakhala kumeneko miyezi isanu ndi umodzi, mpaka adapha amuna onse a ku Edomu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti Yowabu ndi Aisraele onse anakhalako miyezi isanu ndi umodzi, mpaka atawapha amuna onse m'Edomu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yowabu ndi Aisraeli onse anakhala kumeneko miyezi isanu ndi umodzi mpaka anawononga amuna onse a ku Edomu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti Yoabu ndi Aisrayeli onse anakhalako miyezi isanu ndi umodzi, mpaka atawapha amuna onse m'Edomu;