1 Kings 11:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Farao adakomera mtima Hadadi, kotero kuti adampatsa mlamu wake kuti akhale mkazi wake. Mkaziyo anali mbale wake wa mfumukazi Tapenesi wa ku Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Farao anamkomera mtima ndithu Hadadiyo, nampatsa mkazi ndiye mbale wa mkazi wake, mbale wake wa Tapenesi mkazi wamkulu wa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Farao anamukomera mtima Hadadi ndipo anamupatsa mkazi amene anali mngʼono wake wa Mfumukazi Tahipenesi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Farao anamkomera mtima ndithu Hadadiyo, nampatsa mkazi ndiye mbale wa mkazi wace, mbale wace wa Takipenesi mkazi wamkulu wa mfumu.