1 Kings 11:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mkazi wa Hadadiyo adabala mwana wamwamuna dzina lake Genubati, ndipo Tapenesi adalerera Genubati ku nyumba yaufumu. Genubatiyo ankakhala m'nyumba ya Farao pamodzi ndi ana a Farao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mbale wa Tapenesi anamuonera Genubati mwana wake, ameneyo Tapenesi anamletsera kuyamwa m'nyumba ya Farao, ndipo Genubati anakhala m'banja la Farao pamodzi ndi ana amuna a Farao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mngʼono wake wa Tahipenesi anabereka mwana wamwamuna ndipo anamutcha Genubati, amene analeredwa mʼnyumba yaufumu ndi Tahipenesi. Genubatiyo ankakhala limodzi ndi ana a Farao.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mbale wa Takipenesi anamuonera Genubati mwana wace, ameneyo Takipenesi anamletsera kuyamwa m'nyumba ya Farao, ndipo Genubati anakhala m'banja la Farao pamodzi ndi ana amuna a Farao.