1 Kings 11:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Ahiya adagwira mwinjiro watsopano adaavalawo, nkuung'amba m'zidutswa khumi ndi ziŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ahiyayo anagwira chovala chake chatsopano, naching'amba khumi ndi pawiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo Ahiya anagwira mwinjiro watsopano umene anavala ndi kuwungʼamba zidutswa 12.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ahiyayo anagwira cobvala cace catsopano, nacing'amba khumi ndi pawiri.