1 Kings 11:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adauza Yerobowamu kuti, “Iwe utengeko zidutswa khumi. Pakuti Chauta, Mulungu wa Aisraele, akunena kuti, ‘Ndithudi, Ine ndikuchotsa ufumu m'manja mwa Solomoni, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko khumi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati kwa Yerobowamu, Takwaya magawo khumi; popeza atero Yehova Mulungu wa Israele, Taona ndidzaung'amba ufumu m'dzanja la Solomoni ndi kukupatsa iwe mafuko khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono iye anati kwa Yeroboamu, “Tenga zidutswa khumi, pakuti Yehova Mulungu wa Israeli akuti, ‘Taona, Ine ndidzachotsa ufumu mʼdzanja la Solomoni ndipo ndidzakupatsa iwe mafuko khumi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati kwa Yerobiamu, Takwaya magawo khumi; popeza atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Taona ndidzaung'amba ufumu m'dzanja la Solomo ndi kukupatsa iwe mafuko khumi.