1 Kings 11:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ufumuwo ndidzauchotsera m'manja mwa mwana wake, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko khumi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndidzalanda ufumu m'dzanja la mwana wake, ndi kupatsa iwe mafuko khumi amene.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzalanda ufumu mʼdzanja la mwana wake ndipo ndidzakupatsa iwe mafuko khumi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndidzalanda ufumu m'dzanja la mwana wace, ndi kupatsa iwe mafuko khumi amene.