1 Kings 11:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzatenga iweyo Yerobowamu, udzalamulira paliponse pamene mtima wako ufuna, ndipo udzakhala mfumu ya Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzakutenga iwe, ndipo udzachita ufumu monga umo ukhumbira moyo wako, nudzakhala mfumu ya Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma kunena za iwe, ndidzakutenga ndipo udzalamulira chilichonse chimene mtima wako ukukhumba; udzakhala mfumu ya Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakutenga iwe, ndipo udzacita ufumu monga umo ukhumbira moyo wako, nudzakhala mfumu ya Israyeli.