1 Kings 11:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha kuchimwa kwa Solomoniku, ndidzazunza zidzukulu za Davide, koma osati nthaŵi zonse ai.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chifukwa cha ichi ndidzazunza mbumba ya Davide, koma si masiku onse ai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzalanga zidzukulu za Davide chifukwa cha zimenezi, koma osati kwamuyaya.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cifukwa ca ici nelidzazunza mbumba ya Davide, koma si masiku onse ai.