1 Kings 11:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ntchito zina za Solomoni, ndi zonse zimene adachita, ndiponso nzeru zake, zidalembedwa m'buku la Ntchito za Solomoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo machitidwe otsiriza a Solomoni, ndi ntchito zake zonse anazichita, ndi nzeru zake, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a Solomoni?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ntchito zina za Solomoni, zonse zomwe anachita komanso za nzeru zake, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya Solomoni?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo macitidwe otsiriza a Solomo, ndi nchito zace zonse anazicita, ndi nzeru zace, kodi sizilembedwa zimenezo m'buku la madtidwe a Solomo?