1 Kings 11:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Solomoni ankapembedza Asitoreti, mulungu wachikazi wa Asidoni, ndiponso Milikomu, mulungu wonyansa uja wa Aamoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono Solomoni anatsata Asitoreti fano la anthu a Sidoni, ndi Milikomu fano lonyansitsa la Aamoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti iye ankapembedza Asitoreti, mulungu wamkazi wa Asidoni, ndiponso Moleki mulungu wonyansa wa Aamoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono Solomo anatsata Asitoreti fano la anthu a Zidoni, ndi Milikomu fano lonyansitsa la Aamoni.