1 Kings 12:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye mfumuyo idaŵayankha anthuwo mwankhanza. Idanyozera malangizo a madoda aja,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inayankha anthu mau okalipa, naleka uphungu anampangira mandodawo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumuyo inawayankha anthuwo mwankhanza. Kukana malangizo amene akuluakulu anayipatsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inayankha anthu mau okalipa, naleka uphungu anampangira mandodawo,