1 Kings 12:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Rehobowamu adakhala akulamulirabe Aisraele enawo okhala m'mizinda ya Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ana aja a Israele akukhala m'midzi ya Yuda, Rehobowamu anakhalabe mfumu yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Aisraeli amene ankakhala mʼmizinda ya Yuda ankalamuliridwa ndi Rehobowamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kama ana aja a Israyeli akukhala m'midzi ya Yuda, Rehabiamu anakhalabe mfumu yao.