1 Kings 12:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mulungu adadza kwa Semaya, mneneri wake, namlamula kuti, “Ukauze
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mau a Mulungu anafika kwa Semaya mneneri wa Mulungu, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mulungu anayankhula ndi Semaya, munthu wa Mulungu kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mau a Mulungu anafika kwa Semaya mneneri wa Mulungu, nati,