1 Kings 12:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rehobowamu, mwana wa Solomoni, mfumu ya ku Yuda, ndiponso anthu onse a fuko la Yuda ndi la Benjamini kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lankhula kwa Rehobowamu mwana wa Solomoni mfumu ya Yuda, ndi kwa nyumba yonse ya Yuda, ndi Benjamini, ndi kwa anthu otsalawo, nuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nena kwa Rehobowamu mwana wa Solomoni mfumu ya Yuda, kwa nyumba yonse ya Yuda ndi Benjamini, ndiponso kwa anthu ena onse kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lankhula kwa Rehabiamu mwana wa Solomo mfumu ya Yuda, ndi kwa nyumba yonse ya Yuda, ndi Benjamini, ndi kwa anthu otsalawo, nuti,