1 Kings 12:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yerobowamuyo ankaganiza mumtima mwake kuti, “Monga m'mene zilirimu, ufumu udzabwereranso ku banja la Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yerobowamu ananena m'mtima mwake, Ufumuwu udzabwereranso kunyumba ya Davide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yeroboamu anaganiza mu mtima mwake kuti, “Ndithu, ufumuwu udzabwereranso ku nyumba ya Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yerobiamu ananena m'mtima mwace, Ufumuwu udzabwereranso ku nyumba ya Davide.