1 Kings 12:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Yerobowamu adatenga fano lina nkuliika ku Betele, lina nkuliika ku Dani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaimika mmodzi ku Betele, naimika wina ku Dani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Fano lina analiyika ku Beteli ndipo lina analiyika ku Dani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaimika mmodzi ku Beteli, naimika wina ku Dani.