1 Kings 12:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adakamuitana. Choncho Yerobowamu pamodzi ndi anthu onse a ku Israele adadza kwa Rehobowamu namuuza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatuma kukamuitana. Ndipo Yerobowamu ndi msonkhano wonse wa Israele anadza, nalankhulana ndi Rehobowamu, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anthu anayitanitsa Yeroboamu, ndipo iye pamodzi ndi gulu lonse la ku Israeli anapita kwa Rehobowamu ndipo anamuwuza kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatuma akukamuitana. Ndipo Yerobiamu ndi msonkhano wonse wa Israyeli anadza, nalankhulana ndi Rehabiamu, nati,