1 Kings 12:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rehobowamu adauza anthuwo kuti, “Pitani mukabwerenso kuno patapita masiku atatu.” Choncho anthuwo adachoka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye anati kwa iwo, Bamukani, mukagone masiku atatu, pamenepo mukabwera kwa ine. Ndipo anthu anamuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Rehobowamu anayankha kuti, “Pitani, ndipo pakatha masiku atatu, mudzabwerenso.” Choncho anthuwo anapitadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anati kwa iwo, Bamukani, mukagone masiku atatu, pamenepo mukabwera kwa ine. Ndipo anthu anamuka.