1 Kings 13:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mneneriyo adati, “Ine sindingabwerere nanu kapena kukaloŵa m'nyumba mwanu. Sindikadya chakudya kapena kumwa nanu madzi kuno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iye, Sindingabwerere nawe kukalowa kwanu, kapena kudya mkate, kapena kumwa nawe madzi pano;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wa Mulungu uja anati, “Sindingabwerere nanu kapena kudya chakudya kapenanso kumwa madzi kuno.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nan iye, Sindingabwerere nawe kukalowa kwanu, kapena kudya mkate, kapena kumwa nawe madzi pano;