1 Kings 13:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Chauta adandiwuza kuti, ‘Usakadye chakudya kapena kumwa madzi kumeneko, kapenanso kubwerera podzera njira imene udaadzera popita.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti mau a Yehova anadza kwa ine, nati Usakadye mkate, kapena kubwerera njira yomweyo unadzerayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndawuzidwa ndi Yehova kuti, ‘Usadye chakudya kapena kumwa madzi kumeneko kapenanso kubwerera poyenda njira imene unayendamo popita.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti mau a Yehova anadza kwa ine, nati Usakadye mkate, kapena kumwa madzi kumeneko, kapena kubwerera njira yomweyo unadzerayo.