1 Kings 13:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero idabwerera naye limodzi kunyumba kwake, ndipo adakadya namwa madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono anabwerera naye, nakadya kwao, namwa madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho munthu wa Mulungu uja anabwerera naye ndipo anakadya ndi kumwa madzi mʼnyumba mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono anabwerera naye, nakadya kwao, namwa madzi.