1 Kings 13:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
koma mwabwerera, ndipo mwadya ndi kumwa madzi pa malo amene Chauta adakuuzani kuti musakadye chakudya kapena kumwako madzi, mtembo wanu sadzauika m'manda a makolo anu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma unabwerera nudya mkate, ndi kumwa madzi paja pomwe Iye anakuuza, Usakadye mkate, kapena kumwa madzi, mtembo wako tsono sudzaikidwa ku manda a atate ako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe wabwerera ndi kudya chakudya ndiponso kumwa madzi ku malo amene Iye anakuwuza kuti usadye chakudya kapena kumwa madzi. Choncho mtembo wako sadzawuyika mʼmanda a makolo ako.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma unabwerera nudya mkate, ndi kumwa madzi paja pomwe iye anakuuza, Usakadye mkate, kapena kumwa madzi, mtembo wako tsono sudzaikidwa ku manda a atate ako.