1 Kings 13:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho atatha kudya ndi kumwa, adamangirira chishalo pa bulu wa mneneri wa ku Yuda uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunachitika, atadya iye mkate, ndi kumwa madzi, anammangira mbereko pa bulu mneneri amene anambwezayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wa Mulungu atatha kudya ndi kumwa, mneneri amene anamubweza uja anamangirira chishalo pa bulu wa munthu wa Mulunguyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunacitika, atadya iye mkate, ndi kumwa madzi, anammangira mbereko pa buru mneneri amene anambwezayo.