1 Kings 13:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ena amene ankapita mumseumo, adaona mtembo uli gone, mkango utaima pambali pake. Ndipo adapita namakasimbira anzao mu mzinda za zimene adaaona pamseu paja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo onani, anthu anapitapo naona mtembo wogwera m'njiramo, ndi mkango uli chiimire pafupi ndi mtembo, nadzanena m'mudzi m'mene munakhala mneneri wokalamba uja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo taonani, anthu ena amene ankapita mu msewumo anaona mtembowo uli pansi potero, mkango utayima pa mbali pa mtembo uja ndipo anapita nakafotokozera anthu mu mzinda umene mumakhala mneneri wokalamba uja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo onani, anthu anapitapo naona mtembo wogwera m'njiramo, ndi mkango uli ciimire pafupi ndi mtembo, nadzanena m'mudzi m'mene munakhala mneneri wokalamba uja.