1 Kings 13:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, zimene Chauta adalankhulitsa mneneriyo zotemberera guwa la ku Betele ndi nyumba za pa malo achipembedzo zimene zili m'mizinda ya ku Samariya, zidzachitikadi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza mau aja anawafuula mwa mau a Yehova kutemberera guwa la nsembe la ku Betele, ndi kutemberera nyumba zonse za misanje ili m'midzi ya ku Samariya, adzachitika ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti uthenga umene Yehova anamuyankhulitsa, wotsutsana ndi guwa lansembe la ku Beteli ndi nyumba zonse za chipembedzo za mʼmizinda ya ku Samariya, zidzachitika ndithu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza mau aja anawapfuula mwa mau a Yehova kutemberera guwa la nsembe la ku Beteli, ndi kutemberera nyumba zonse za misanje iri m'midzi ya ku Samariya, adzacitika ndithu.