1 Kings 13:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mneneri wa Mulungu uja adauza mfumu kuti, “Ngakhale mundipatse theka la chuma chanu, sindikadya chakudya chilichonse kapena kumwa madzi kuno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munthu wa Mulungu ananena ndi mfumu, Mungakhale mundigawira pakati ndi pakati nyumba yanu, sindilowa kwa inu, kapena kudya mkate, kapena kumwa madzi kuno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma munthu wa Mulunguyo anayankha mfumu kuti, “Ngakhale mutandipatsa theka la chuma chanu, sindingapite nanu, kapena kudya chakudya, kapenanso kumwa madzi kuno.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munthu wa Mulungu ananena ndi mfumu, Mungakhale mundigawira pakati ndi pakati nyumba yanu, sindilowa kwa inu, kapena kudya mkate, kapena kumwa madzi kuno.