1 Kings 13:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Chauta adandilamula kuti, ‘Usakadye chakudya chilichonse, kapena kumwa madzi, kapenanso kudzera njira yomwe udaadzera kale pobwera.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti potero ndinalamulidwa ndi mau a Yehova, ndi kuti, Usakadye mkate, kapena kumwa madzi, kapena kubwerera njira yomweyo unadzerayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova anandilamula kuti, ‘Usakadye chakudya kapena kumwa madzi kapena kubwerera podzera njira imene unayendamo kale.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti potero ndinalamulidwa ndi mau a Yehova, ndi kuti, Usakadye mkate, kapena kumwa madzi, kapena kubwerera njira yomweyo unadzerayo.