1 Kings 14:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi imeneyo Abiya, mwana wa Yerobowamu, adayamba kudwala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nthawi yomweyo Abiya mwana wa Yerobowamu anadwala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi imeneyo Abiya mwana wa Yeroboamu anayamba kudwala,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nthawi yomweyo Abiya mwana wa Yerobiamu anadwala.