1 Kings 14:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono nyamuka, upite kunyumba kwako. Phazi lako likangoponda mumzindamo, mwanayo adzafa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tanyamuka tsono, numuke kwanu; pakulowa mapazi ako m'mudzi mwanayo adzatsirizika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndipo iwe nyamuka, bwerera ku nyumba kwako. Phazi lako likadzangoponda mu mzindamo, mwanayo adzamwalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tanyamuka tsono, numuke kwanu; pakulowa mapazi ako m'mudzi mwanayo adzatsirizika.