1 Kings 14:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele adamuika, nalira maliro ake, monga momwe Chauta adaanenera kudzera mwa mneneri Ahiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamuika, namlira Aisraele, monga mwa mau a Yehova anawalankhula pa dzanja la mtumiki wake Ahiya mneneri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli anamuyika mʼmanda, ndipo onse analira maliro ake, monga momwe Yehova ananenera kudzera mwa mtumiki wake, mneneri Ahiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamuika, namlira Aisrayeli, monga mwa mau a Yehova anawalankhula pa dzanja la mtumiki wace Ahiya mneneri.