1 Kings 14:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imene Yerobowamu adakhala mfumu idakwana zaka makumi aŵiri. Ndipo adamwalira, naikidwa m'manda. Pambuyo pake Nadabu mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo masiku akukhala Yerobowamu mfumu anali zaka makumi awiri mphambu ziwiri, nagona iye ndi makolo ake, nalowa ufumu m'malo mwake Nadabu mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye analamulira zaka 22 ndipo anamwalira nayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake. Ndipo Nadabu mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo masiku akukhala Yerobiamu mfumu anali zaka makumi awiri mphambu ziwiri, nagona iye kwa makolo ace, nalowa ufumu m'malo mwace Nadabu mwana wace.